Ndipo maguy don't let your love partner, makamaka girls, osamayilora idzikhala kwambiri pa social media especially pa tiktok paja... These girls get carried away so easily ndi maguyz apa Tiktok I donno why koma izizi ndi fact.
Dzulo madzulo I was giving my dogs some food nde ndinawona kazizi and then mtalowa mnyumba mutu unayamba kundiwawa, nde mnazaganiza zamakolo zija amati kazizi amatha kubwera pakhomo pakakhala maliro😂koma maguy dzulo ndalapa😭😭😂 sindinakhulupirireko pemphero ngati dzulo😂😂😭
Yesterday I promised this other girl some money, Komatu girls mumapanga communicate bwino when you've been promised to be given something, mpaka kundifunsatu ati "what are you going to eat mawa" eh eh😭😂
Guys let us dream big, of course pali zinthu zina umaziopera patali kuti sizingatheke just because of where we coming from, komano kumangokumbukira kuti palibe bill yomwe Mulungu sangakwanise kulipira.🤝🏽