Accused Number One π²πΌ
2 years
Ku Chilumba garrison agwira ali ndi military ID
Name Daniel Kachimanga
Alinso ndi driving license, Name Stanley Kachimanga, ati dzinalo ndilamkuluwake koma nkhopeyo pali iyeyo. Wagwidwa chifukwa anakanika kudziwa ma command a MDF.