Koma azimai masiku ano nde anatha ah, yesterday my Mom called me around 11 pm, kuti my little bro wakomoka and waledzera nde akufuna azipita naye ku hospa cause sanadye. I was like wa Blacker ameneyo kagoneni adzuka. This morning akuimba kuti wadzuka nde akumuphikira ah ah๐๐
My housemate wangochoka ku groove mma 6 mu, kufikila ku bathroom apa wanyamuka kupita ku church ๐๐ ndikudikila andiuze kuti chachitika ndi chani๐
Anthu okonda kuwerenga inu, pali ma novels awa going at a give away proce of MWK1,500 each. Contact me tikupangirani. 0884126671
Please rt.
@marinna_issat
tithandizeni๐
Did this job for adha enaake, guy's very happy with it. This morning, he came to make the final payment, kenaka wandipasa ka 10k ati ndikamwe zanga zija.... atafika kwao waimbaso kuti akutuma wa vep abweresa something small... ๐ฅ
The promo y'all X people gave to
@Crispy_malawi
new project Was so exquisite, imagine giving that Hype to atleast 5 or more ๐ฒ๐ผ Artist's this can make a big change in our industry. ๐ฏ
Selling Chickens in Blantyre, free deliveries ku
Limbe and Blantyre.
They're going at MWK5,500.
They can come dressed or not at that price.
Contact: 0884126671
Please rt.
So lero ndangonva kuti some catholic institution anapanga book Spe, nde cause anafikako ma guys 11 anawapasa Office ya Father kuti adekhe kaye kudikira performance. Ma guy akuti anamenya hotbox tu mu office mwa father๐๐๐๐
She kept me in her womb for 9 months, she stayed 3 months + in a hospital nditapsa, she managed to pay my uni tuition and upkeep from year 1 second semester mpaka kumaliza school after the death of dad and etcetera... I'll always love that womanโค๏ธ