Amangosowa ndi munthu omuwuza pop young kuti ku MW kuno munthu sumatchuka kawiri. I mean the guy had a chance to shine with a big brand koma ayi he signed out. This is why every song he does is a flop!!! Pop Youngs career inatha isanayambike. And you all mukungomupopa zabodza💔.