Eeh guys ndimafa straight 😅😅😅pano am getting back to my damn feets..apa tili kae pa drip number 3 komaso Lunatic amuuza asadye mpaka mawa paliso ma procedures ena ena omwe tipange..Lunatic vomited more than 2 litre blood
Thank you guys for your healing messages
Ndikukhala ku South Africa mopanda mapepala ndikukhala mopanda wina aliyense kundivutitsa, nde iwe pano data yanga, phone yanga nde ufuna uzindiuza zochita aaah Panyo
Let's fix this app .
@Naymore43
Vuto mufuna anthu azikuopani ngati muli ndi ma shares ku X ...mxiew anthu aziopa kuika ma opinions chifukwa choti muwamangitsa..zomangitsa anthu muzaona polekera one day
Akuti MCP ndiyakatangale people wants change koma akufuna kuipanga replace ndi chipani chinaso chakatangale nde pamenepo change ili pati?🤣🤣amalawi kuganiza ngati nkhumba 🤣🤣🤣
Dzulo ndikuyenda mu Limbe, nnadzidzimuka ntamuona Lunatic, Kodi mesa ali ku south africa uyu? Ndipite pafupi ndikapange confirm, koma khungu lake chimodzi modzi ndima picture ake, ndinayamba kuvaya konko kuti ndikamujambule,
Linali thumba la mbatata, sanali Lunatic
VYBZ Kartel looks bloated & unfit here cos he developed kidney failure, pulmonary edema (swollen lungs), dermatitis (inflammation of the skin) & testicular edema (swollen testicles) during his 12 years in prison.
His failing health was grounds for his early discharge. Even his