Timafananiza SPE ndi charisma osati SPE ndi gang ya charisma 😂😂😂 show yaku mzuni nalikonko anthu tinapita kukaona yachina gwambizo osati charisma.....za charisma tajowa poti tinali titaledzera kale😭😂😂😂😂😂😂😂
Akatolika mutsutsa Koma Driemo is better than Kell Kay...... sinkhaniso yoti Kell Kay wakhalitsa mu industry ayih sinkhaniso yama looks ayih koma Driemo amayimba bho than Kell Kay 🤝 Olo mukwiye 😂😂😂😂😂
Masten was going through my Airtel transactions akhumudwa ati ndalama ndungothera akazi avekere
Ndalama ukungothera "PAWAPAY" ndiwakuti nkazi ameneyu.... Ndiwauze?
Facts coz ineso I feel like gwamba is overrated 🤣🤣🤣🤣koma sindikhala busy Ku comment section convincing everyone coz imeneyo nde hate 🤣🤣🤣 tisiyeni tizivera SPE amaphika bho🐐😂
I can't talk about how exceptional Spe is without being cooked.. Tiyeni tipange support ma artist athuwo without comparing them. If I feel like he's the GOAT then that's according to me. And if you don't like him it's ok. Zinthuzi zili ngat chakudya timakonda zosiyana. 🙂👍🏾